Yesaya 37:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000. Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:36 Nsanja ya Olonda,6/1/1993, tsa. 62/1/1991, tsa. 171/15/1988, tsa. 18
36 Ndiyeno mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000. Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+