Yesaya 37:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pamene Senakeribu ankaweramira mulungu wake Nisiroki mʼkachisi, ana ake Adarameleki ndi Sarezere anamupha ndi lupanga+ nʼkuthawira kudziko la Ararati.+ Kenako mwana wake Esari-hadoni+ anakhala mfumu mʼmalo mwake. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:38 Nsanja ya Olonda,4/1/2003, tsa. 11
38 Pamene Senakeribu ankaweramira mulungu wake Nisiroki mʼkachisi, ana ake Adarameleki ndi Sarezere anamupha ndi lupanga+ nʼkuthawira kudziko la Ararati.+ Kenako mwana wake Esari-hadoni+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.