Yesaya 38:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndadzitonthoza mpaka mʼmawa. Mofanana ndi mkango, iye akungokhalira kuphwanya mafupa anga onse.Kuyambira mʼmawa mpaka usiku mukuchititsa kuti ndithe pangʼonopangʼono.+
13 Ndadzitonthoza mpaka mʼmawa. Mofanana ndi mkango, iye akungokhalira kuphwanya mafupa anga onse.Kuyambira mʼmawa mpaka usiku mukuchititsa kuti ndithe pangʼonopangʼono.+