Yesaya 39:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Hezekiya atamva zimenezi anauza Yesaya kuti: “Mawu a Yehova amene mwanenawa ndi abwino.” Anapitiriza kuti: “Chifukwa mʼmasiku anga mukhala bata* ndi mtendere.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:8 Yesaya 1, tsa. 397
8 Hezekiya atamva zimenezi anauza Yesaya kuti: “Mawu a Yehova amene mwanenawa ndi abwino.” Anapitiriza kuti: “Chifukwa mʼmasiku anga mukhala bata* ndi mtendere.”+