Yesaya 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chigwa chilichonse chikwezedwe mʼmwamba,Ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zitsitsidwe. Malo okumbikakumbika asalazidwe,Ndipo malo azitunda akhale chigwa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:4 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2023, tsa. 15 Yesaya 1, ptsa. 399-401
4 Chigwa chilichonse chikwezedwe mʼmwamba,Ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zitsitsidwe. Malo okumbikakumbika asalazidwe,Ndipo malo azitunda akhale chigwa.+