-
Yesaya 40:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Fuula mwamphamvu,
Iwe mkazi amene ukubweretsa uthenga wabwino wonena za Yerusalemu.
Fuula, usachite mantha.
Lengeza kumizinda ya ku Yuda kuti: “Mulungu wanu ali nanu.”+
-