Yesaya 40:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo ali ngati mbewu zimene zangodzalidwa kumene,Ali ngati mbewu zimene zangofesedwa kumene,Thunthu lawo langoyamba kumene kuzika mizu munthaka.Mphepo yawawomba nʼkuumaNdipo auluzika ndi mphepo ngati mapesi.+
24 Iwo ali ngati mbewu zimene zangodzalidwa kumene,Ali ngati mbewu zimene zangofesedwa kumene,Thunthu lawo langoyamba kumene kuzika mizu munthaka.Mphepo yawawomba nʼkuumaNdipo auluzika ndi mphepo ngati mapesi.+