Yesaya 40:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nʼchifukwa chiyani iwe Yakobo, komanso nʼchifukwa chiyani iwe Isiraeli ukunena kuti,‘Yehova sakuona zimene zikuchitika pa moyo wanga,Ndipo Mulungu akunyalanyaza zinthu zopanda chilungamo zimene zikundichitikiraʼ?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:27 Nsanja ya Olonda,1/15/2007, tsa. 9 Yesaya 1, ptsa. 411-413, 415
27 Nʼchifukwa chiyani iwe Yakobo, komanso nʼchifukwa chiyani iwe Isiraeli ukunena kuti,‘Yehova sakuona zimene zikuchitika pa moyo wanga,Ndipo Mulungu akunyalanyaza zinthu zopanda chilungamo zimene zikundichitikiraʼ?+