Yesaya 41:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe amene ndinakutenga kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+Ndiponso iwe amene ndinakuitana kuchokera kumadera akutali a dziko lapansi. Ndinakuuza kuti, ‘Iwe ndiwe mtumiki wanga.+Ndakusankha ndipo sindinakutaye.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:9 Yesaya 2, ptsa. 22-23
9 Iwe amene ndinakutenga kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+Ndiponso iwe amene ndinakuitana kuchokera kumadera akutali a dziko lapansi. Ndinakuuza kuti, ‘Iwe ndiwe mtumiki wanga.+Ndakusankha ndipo sindinakutaye.+