Yesaya 41:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+Chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano akuthwa konsekonse. Udzapondaponda mapiri nʼkuwaphwanyaNdipo zitunda udzazisandutsa mankhusu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:15 Yesaya 2, ptsa. 24-25
15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+Chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano akuthwa konsekonse. Udzapondaponda mapiri nʼkuwaphwanyaNdipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.