Yesaya 41:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Udzapeta mapiri ndi zitundazoNdipo mphepo idzaziuluza.Mphepo yamkuntho idzazimwaza. Iweyo udzasangalala chifukwa cha Yehova,+Ndipo udzadzitama chifukwa cha Woyera wa Isiraeli.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:16 Yesaya 2, ptsa. 24-25
16 Udzapeta mapiri ndi zitundazoNdipo mphepo idzaziuluza.Mphepo yamkuntho idzazimwaza. Iweyo udzasangalala chifukwa cha Yehova,+Ndipo udzadzitama chifukwa cha Woyera wa Isiraeli.”+