Yesaya 41:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Anthu ovutika ndi osauka akufunafuna madzi, koma sakuwapeza. Lilime lawo lauma chifukwa cha ludzu.+ Ineyo Yehova ndidzawayankha.+ Ineyo Mulungu wa Isiraeli, sindidzawasiya.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:17 Yesaya 2, ptsa. 25-26
17 “Anthu ovutika ndi osauka akufunafuna madzi, koma sakuwapeza. Lilime lawo lauma chifukwa cha ludzu.+ Ineyo Yehova ndidzawayankha.+ Ineyo Mulungu wa Isiraeli, sindidzawasiya.+