Yesaya 41:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzachititsa kuti mitsinje yamadzi iyende mʼmapiri opanda zomera zilizonse+Komanso kuti akasupe atuluke mʼzigwa.+ Chipululu ndidzachisandutsa dambo lamadziNdipo dziko lopanda madzi ndidzalisandutsa akasupe amadzi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:18 Yesaya 2, ptsa. 25-26
18 Ndidzachititsa kuti mitsinje yamadzi iyende mʼmapiri opanda zomera zilizonse+Komanso kuti akasupe atuluke mʼzigwa.+ Chipululu ndidzachisandutsa dambo lamadziNdipo dziko lopanda madzi ndidzalisandutsa akasupe amadzi.+