Yesaya 41:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndidzachita zimenezi kuti anthu onse aone ndipo adziwe,Amve ndiponso azindikireKuti dzanja la Yehova ndi limene lachita zimenezi,Ndiponso kuti Woyera wa Isiraeli ndi amene wachititsa zimenezi.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:20 Yesaya 2, ptsa. 25-26
20 Ndidzachita zimenezi kuti anthu onse aone ndipo adziwe,Amve ndiponso azindikireKuti dzanja la Yehova ndi limene lachita zimenezi,Ndiponso kuti Woyera wa Isiraeli ndi amene wachititsa zimenezi.”+