Yesaya 41:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Tipatseni umboni ndipo mutiuze zinthu zimene zidzachitike. Tiuzeni zokhudza zinthu zakale,*Kuti tiziganizire mozama nʼkudziwa tsogolo lake. Kapena mutiuze zinthu zimene zikubwera.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:22 Yesaya 2, ptsa. 26-28 Nsanja ya Olonda,6/15/1993, tsa. 142/1/1988, tsa. 14
22 “Tipatseni umboni ndipo mutiuze zinthu zimene zidzachitike. Tiuzeni zokhudza zinthu zakale,*Kuti tiziganizire mozama nʼkudziwa tsogolo lake. Kapena mutiuze zinthu zimene zikubwera.+