Yesaya 41:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Onsewo ndi opanda ntchito.* Ntchito zawo ndi zopanda pake. Mafano awo opangidwa ndi zitsulo* ali ngati mphepo ndipo ndi opanda ntchito.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:29 Yesaya 2, tsa. 29
29 Onsewo ndi opanda ntchito.* Ntchito zawo ndi zopanda pake. Mafano awo opangidwa ndi zitsulo* ali ngati mphepo ndipo ndi opanda ntchito.+