Yesaya 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taonani, zinthu zimene ndinaneneratu kalekale zachitika,Tsopano ndikulengeza zinthu zatsopano. Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:9 Yesaya 2, tsa. 41
9 Taonani, zinthu zimene ndinaneneratu kalekale zachitika,Tsopano ndikulengeza zinthu zatsopano. Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+