Yesaya 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+Mʼtamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+Inu nonse amene mumadalira nyanja komanso zonse zimene zimakhala mmenemo,Inu zilumba ndi anthu amene amakhala mʼzilumbazo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:10 Nsanja ya Olonda,12/15/2001, tsa. 25 Yesaya 2, ptsa. 41-42
10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+Mʼtamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi,+Inu nonse amene mumadalira nyanja komanso zonse zimene zimakhala mmenemo,Inu zilumba ndi anthu amene amakhala mʼzilumbazo.+