Yesaya 42:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amene akudalira zifaniziro zosema,Amene akuuza zifaniziro zachitsulo* kuti: “Ndinu milungu yathu,”+Adzathawa ndipo adzachita manyazi kwambiri. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:17 Yesaya 2, tsa. 44
17 Anthu amene akudalira zifaniziro zosema,Amene akuuza zifaniziro zachitsulo* kuti: “Ndinu milungu yathu,”+Adzathawa ndipo adzachita manyazi kwambiri.