Yesaya 42:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu amene muli ndi vuto losamva, mvetserani.Inu amene muli ndi vuto losaona, yangʼanani kuti muone.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:18 Yesaya 2, ptsa. 44-45
18 Inu amene muli ndi vuto losamva, mvetserani.Inu amene muli ndi vuto losaona, yangʼanani kuti muone.+