Yesaya 42:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma awa ndi anthu amene katundu wawo wabedwa komanso kulandidwa.+Onse agwera mʼmaenje amene sangathe kutulukamo ndipo atsekeredwa mʼndende.+ Iwo atengedwa popanda wowapulumutsa,+Agwidwa popanda wonena kuti: “Bwererani nawo!” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:22 Yesaya 2, tsa. 45
22 Koma awa ndi anthu amene katundu wawo wabedwa komanso kulandidwa.+Onse agwera mʼmaenje amene sangathe kutulukamo ndipo atsekeredwa mʼndende.+ Iwo atengedwa popanda wowapulumutsa,+Agwidwa popanda wonena kuti: “Bwererani nawo!”