-
Yesaya 42:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndi ndani pakati panu amene adzamvetsere zinthu zimenezi?
Ndi ndani amene adzatchere khutu ndi kumvetsera zinthu zimene zidzamuthandize mʼtsogolo?
-