-
Yesaya 42:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ndi ndani wachititsa kuti Yakobo alandidwe katundu wake
Ndiponso kupereka Isiraeli kwa anthu olanda?
Kodi si Yehova amene iwo amuchimwira?
-