Yesaya 42:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Mulungu anapitiriza kuwakhuthulira ukali ndi mkwiyo wake,Anawabweretsera nkhondo yoopsa.+ Moto unapsereza chilichonse chimene anali nacho, koma iwo sanalabadire.+ Motowo unapitiriza kuwawotcha koma iwo sizinawakhudze.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:25 Yesaya 2, tsa. 45
25 Choncho Mulungu anapitiriza kuwakhuthulira ukali ndi mkwiyo wake,Anawabweretsera nkhondo yoopsa.+ Moto unapsereza chilichonse chimene anali nacho, koma iwo sanalabadire.+ Motowo unapitiriza kuwawotcha koma iwo sizinawakhudze.+