Yesaya 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wako,Woyera wa Isiraeli, Mpulumutsi wako. Ndapereka Iguputo kuti akhale dipo* lako.Ndaperekanso Itiyopiya ndi Seba mʼmalo mwa iwe. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:3 Yesaya 2, ptsa. 48-49
3 Chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wako,Woyera wa Isiraeli, Mpulumutsi wako. Ndapereka Iguputo kuti akhale dipo* lako.Ndaperekanso Itiyopiya ndi Seba mʼmalo mwa iwe.