Yesaya 43:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Usachite mantha chifukwa ine ndili ndi iwe.+ Ndidzabweretsa mbadwa* zako kuchokera kumʼmawa,Ndipo ndidzakusonkhanitsani pamodzi kuchokera kumadzulo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:5 Yesaya 2, tsa. 50 Nsanja ya Olonda,1/1/1994, ptsa. 3-4
5 Usachite mantha chifukwa ine ndili ndi iwe.+ Ndidzabweretsa mbadwa* zako kuchokera kumʼmawa,Ndipo ndidzakusonkhanitsani pamodzi kuchokera kumadzulo.+