Yesaya 43:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzauza kumpoto kuti, ‘Abwezere kwawo!’+ Ndipo ndidzauza kumʼmwera kuti, ‘Usawakanize. Bweretsa ana anga aamuna kuchokera kutali komanso ana anga aakazi kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:6 Yesaya 2, tsa. 50
6 Ndidzauza kumpoto kuti, ‘Abwezere kwawo!’+ Ndipo ndidzauza kumʼmwera kuti, ‘Usawakanize. Bweretsa ana anga aamuna kuchokera kutali komanso ana anga aakazi kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:6 Yesaya 2, tsa. 50