Yesaya 43:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Chifukwa cha inu, ndidzatumiza asilikali ku Babulo ndipo adzagwetsa zotsekera mʼmageti,+Komanso Akasidi adzalira chifukwa chopanikizika, ali mʼsitima zawo zapamadzi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:14 Yesaya 2, ptsa. 54-55
14 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Chifukwa cha inu, ndidzatumiza asilikali ku Babulo ndipo adzagwetsa zotsekera mʼmageti,+Komanso Akasidi adzalira chifukwa chopanikizika, ali mʼsitima zawo zapamadzi.+