Yesaya 43:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndine Yehova, Woyera wanu,+ Mlengi wa Isiraeli+ ndiponso Mfumu yanu.”+