Yesaya 43:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amene amatsogolera magaleta ankhondo ndi mahatchi,+Gulu lankhondo pamodzi ndi asilikali amphamvu, wanena kuti: “Iwo adzagona pansi ndipo sadzadzukanso.+ Adzazimitsidwa ngati chingwe cha nyale.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:17 Yesaya 2, ptsa. 54-55
17 Amene amatsogolera magaleta ankhondo ndi mahatchi,+Gulu lankhondo pamodzi ndi asilikali amphamvu, wanena kuti: “Iwo adzagona pansi ndipo sadzadzukanso.+ Adzazimitsidwa ngati chingwe cha nyale.”