Yesaya 43:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Taonani! Ndikupanga chinthu chatsopano.+Ngakhale panopa chikuonekera. Kodi simukuchizindikira? Ndidzapanga njira mʼchipululu,+Ndipo mitsinje idzadutsa mʼchipululumo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:19 Yesaya 2, ptsa. 55-57, 60
19 Taonani! Ndikupanga chinthu chatsopano.+Ngakhale panopa chikuonekera. Kodi simukuchizindikira? Ndidzapanga njira mʼchipululu,+Ndipo mitsinje idzadutsa mʼchipululumo.+