Yesaya 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa ndidzapatsa madzi munthu waludzu*+Ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi oyenda pamalo ouma. Ndidzatsanulira mzimu wanga pa ana ako*+Komanso madalitso anga pa mbadwa zako. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:3 Yesaya 2, tsa. 64
3 Chifukwa ndidzapatsa madzi munthu waludzu*+Ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi oyenda pamalo ouma. Ndidzatsanulira mzimu wanga pa ana ako*+Komanso madalitso anga pa mbadwa zako.