Yesaya 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu adzati: “Ine ndine wa Yehova.”+ Wina adzadzipatsa dzina la Yakobo,Winanso adzalemba padzanja lake kuti: “Ndine wa Yehova.” Ndipo adzatenga dzina la Isiraeli.’ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:5 Yesaya 2, tsa. 64
5 Munthu adzati: “Ine ndine wa Yehova.”+ Wina adzadzipatsa dzina la Yakobo,Winanso adzalemba padzanja lake kuti: “Ndine wa Yehova.” Ndipo adzatenga dzina la Isiraeli.’