Yesaya 44:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi ndi ndani amene angafanane ndi ine?+ Ayankhe molimba mtima ndi kupereka umboni wake kwa ine.+ Kuyambira nthawi imene ndinakhazikitsa anthu akalekale,Iwo anene zinthu zimene zichitike posachedwapaNdi zimene zidzachitike mʼtsogolo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:7 Yesaya 2, ptsa. 64-65
7 Kodi ndi ndani amene angafanane ndi ine?+ Ayankhe molimba mtima ndi kupereka umboni wake kwa ine.+ Kuyambira nthawi imene ndinakhazikitsa anthu akalekale,Iwo anene zinthu zimene zichitike posachedwapaNdi zimene zidzachitike mʼtsogolo.