Yesaya 44:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu onse opanga zifaniziro zosema ndi opanda pake,Ndipo mafano awo amene amawanyadira ndi opanda phindu.+ Mofanana ndi mboni zawo, mafanowo saona chilichonse ndipo sadziwa chilichonse,+Choncho anthu amene anawapanga adzachititsidwa manyazi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:9 Yesaya 2, tsa. 66
9 Anthu onse opanga zifaniziro zosema ndi opanda pake,Ndipo mafano awo amene amawanyadira ndi opanda phindu.+ Mofanana ndi mboni zawo, mafanowo saona chilichonse ndipo sadziwa chilichonse,+Choncho anthu amene anawapanga adzachititsidwa manyazi.+