Yesaya 44:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi pali aliyense wopusa amene angafike popanga mulungu kapena fano lopangidwa ndi chitsulo chosungunula,*Lomwe ndi lopanda phindu?+
10 Kodi pali aliyense wopusa amene angafike popanga mulungu kapena fano lopangidwa ndi chitsulo chosungunula,*Lomwe ndi lopanda phindu?+