Yesaya 44:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anzake onse adzachititsidwa manyazi,+ Amisiriwo ndi anthu basi. Onsewo asonkhane pamodzi ndipo akhale pamalo awo. Adzachita mantha ndipo onsewo adzachititsidwa manyazi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:11 Yesaya 2, tsa. 66
11 Anzake onse adzachititsidwa manyazi,+ Amisiriwo ndi anthu basi. Onsewo asonkhane pamodzi ndipo akhale pamalo awo. Adzachita mantha ndipo onsewo adzachititsidwa manyazi.