Yesaya 44:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wosula zitsulo akugwiritsa ntchito chida chake posula chitsulo chimene wachiwotcha pamoto wamakala. Akuchiwongola ndi hamala,Akuchisula ndi dzanja lake lamphamvu.+ Kenako wamva njala ndipo mphamvu zake zatha.Sanamwe madzi ndipo watopa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:12 Yesaya 2, ptsa. 66-67
12 Munthu wosula zitsulo akugwiritsa ntchito chida chake posula chitsulo chimene wachiwotcha pamoto wamakala. Akuchiwongola ndi hamala,Akuchisula ndi dzanja lake lamphamvu.+ Kenako wamva njala ndipo mphamvu zake zatha.Sanamwe madzi ndipo watopa.