Yesaya 44:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma mtengo wotsalawo wapangira mulungu, wapangira chifaniziro chake chosema. Akuchiweramira komanso kuchilambira. Akupemphera kwa chifanizirocho kuti: “Ndipulumutseni, chifukwa ndinu mulungu wanga.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:17 Yesaya 2, ptsa. 67-68
17 Koma mtengo wotsalawo wapangira mulungu, wapangira chifaniziro chake chosema. Akuchiweramira komanso kuchilambira. Akupemphera kwa chifanizirocho kuti: “Ndipulumutseni, chifukwa ndinu mulungu wanga.”+