-
Yesaya 44:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Iye akudya phulusa.
Mtima wake umene wapusitsidwa wamusocheretsa.
Iye sangathe kudzipulumutsa kapena kunena kuti:
“Kodi chinthu chimene chili mʼdzanja langa lamanjachi si chabodza?”
-