Yesaya 44:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Kumbukira zinthu zimenezi iwe Yakobo ndiponso iwe Isiraeli,Chifukwa ndiwe mtumiki wanga. Ine ndinakupanga ndipo iweyo ndiwe mtumiki wanga.+ Iwe Isiraeli, ine sindidzakuiwala.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:21 Yesaya 2, ptsa. 69-70
21 “Kumbukira zinthu zimenezi iwe Yakobo ndiponso iwe Isiraeli,Chifukwa ndiwe mtumiki wanga. Ine ndinakupanga ndipo iweyo ndiwe mtumiki wanga.+ Iwe Isiraeli, ine sindidzakuiwala.+