Yesaya 44:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndine amene ndimachititsa mawu a mtumiki wanga kuti akwaniritsidweNdiponso amene ndimakwaniritsa mawu onse amene amithenga anga analosera.+Ndine amene ndikunena za Yerusalemu kuti, ‘Muzidzakhala anthu.’+ Ndikunenanso za mizinda ya ku Yuda kuti, ‘Idzamangidwanso,+Ndipo ndidzakonza malo ake amene anawonongedwa.’+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:26 Yesaya 2, ptsa. 70-71 Ulosi wa Danieli, ptsa. 150-151 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, ptsa. 8-9
26 Ndine amene ndimachititsa mawu a mtumiki wanga kuti akwaniritsidweNdiponso amene ndimakwaniritsa mawu onse amene amithenga anga analosera.+Ndine amene ndikunena za Yerusalemu kuti, ‘Muzidzakhala anthu.’+ Ndikunenanso za mizinda ya ku Yuda kuti, ‘Idzamangidwanso,+Ndipo ndidzakonza malo ake amene anawonongedwa.’+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:26 Yesaya 2, ptsa. 70-71 Ulosi wa Danieli, ptsa. 150-151 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, ptsa. 8-9