Yesaya 45:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndidzakupatsa chuma chimene chili mumdimaNdiponso chuma chimene chabisidwa mʼmalo achinsinsi,+Kuti udziwe kuti ine ndine Yehova,Mulungu wa Isiraeli, amene ndikukuitana pokutchula dzina lako.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:3 Yesaya 2, ptsa. 76-79 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, tsa. 119/1/1987, ptsa. 26-27
3 Ndidzakupatsa chuma chimene chili mumdimaNdiponso chuma chimene chabisidwa mʼmalo achinsinsi,+Kuti udziwe kuti ine ndine Yehova,Mulungu wa Isiraeli, amene ndikukuitana pokutchula dzina lako.+