Yesaya 45:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova, Woyera wa Isiraeli+ ndiponso amene anamuumba, wanena kuti: “Kodi ukukaikira mawu anga okhudza zinthu zimene zikubweraNdipo ukundilamula zinthu zokhudza ana anga+ komanso ntchito ya manja anga? Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:11 Yesaya 2, ptsa. 85-86
11 Yehova, Woyera wa Isiraeli+ ndiponso amene anamuumba, wanena kuti: “Kodi ukukaikira mawu anga okhudza zinthu zimene zikubweraNdipo ukundilamula zinthu zokhudza ana anga+ komanso ntchito ya manja anga?