Yesaya 45:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Isiraeli adzapulumutsidwa ndi Yehova ndipo chipulumutso chake chidzakhala chosatha.+ Inu simudzachititsidwa manyazi kapena kunyozeka mpaka kalekale.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:17 Yesaya 2, tsa. 88
17 Koma Isiraeli adzapulumutsidwa ndi Yehova ndipo chipulumutso chake chidzakhala chosatha.+ Inu simudzachititsidwa manyazi kapena kunyozeka mpaka kalekale.+