Yesaya 45:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mbadwa* zonse za Isiraeli zidzaona kuti zinachita bwino kutumikira Yehova,+Ndipo zidzadzitama chifukwa cha zinthu zimene iye anazichitira.’” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:25 Yesaya 2, tsa. 91
25 Mbadwa* zonse za Isiraeli zidzaona kuti zinachita bwino kutumikira Yehova,+Ndipo zidzadzitama chifukwa cha zinthu zimene iye anazichitira.’”