Yesaya 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Beli wawerama+ ndipo Nebo wagwada. Mafano awo anyamulidwa ndi nyama, nyama zonyamula katundu.+Mafanowo ali ngati katundu wolemera kwa nyama zotopa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:1 Yesaya 2, ptsa. 93-95
46 Beli wawerama+ ndipo Nebo wagwada. Mafano awo anyamulidwa ndi nyama, nyama zonyamula katundu.+Mafanowo ali ngati katundu wolemera kwa nyama zotopa.