Yesaya 46:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inu anyumba ya Yakobo ndimvetsereni, komanso inu nonse otsala a mʼnyumba ya Isiraeli,+Inu amene ndakuthandizani kuyambira pamene munabadwa ndiponso kukunyamulani kuyambira pamene munatuluka mʼmimba.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:3 Yesaya 2, tsa. 96
3 “Inu anyumba ya Yakobo ndimvetsereni, komanso inu nonse otsala a mʼnyumba ya Isiraeli,+Inu amene ndakuthandizani kuyambira pamene munabadwa ndiponso kukunyamulani kuyambira pamene munatuluka mʼmimba.+