Yesaya 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale mudzakalambe, ine ndidzakhala chimodzimodzi.+Ngakhale tsitsi lanu lidzachite imvi, ine ndidzapitiriza kukunyamulani. Ndidzakunyamulani, kukuthandizani komanso kukupulumutsani ngati mmene ndakhala ndikuchitira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:4 Yesaya 2, tsa. 97
4 Ngakhale mudzakalambe, ine ndidzakhala chimodzimodzi.+Ngakhale tsitsi lanu lidzachite imvi, ine ndidzapitiriza kukunyamulani. Ndidzakunyamulani, kukuthandizani komanso kukupulumutsani ngati mmene ndakhala ndikuchitira.+