Yesaya 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pali anthu amene amakhuthula golide mʼzikwama zawo.Amayeza siliva pasikelo. Iwo amalemba ganyu mmisiri wa zitsulo ndipo amapanga mulungu ndi zinthu zimenezi.+ Kenako anthuwo amayamba kumuweramira ndi kumulambira.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:6 Yesaya 2, tsa. 99
6 Pali anthu amene amakhuthula golide mʼzikwama zawo.Amayeza siliva pasikelo. Iwo amalemba ganyu mmisiri wa zitsulo ndipo amapanga mulungu ndi zinthu zimenezi.+ Kenako anthuwo amayamba kumuweramira ndi kumulambira.*+